Genesis 21:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abimeleki adamufunsa kuti “Chifukwa chiyani mukuchita zimenezi?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abimeleki anati kwa Abrahamu, Nanga anaankhosa akazi asanu ndi awiri amene wapatula pa okha?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo Abimeleki anafunsa Abrahamu, “Kodi tanthauzo lake la ana ankhosa aakazi asanu ndi awiri amene wawapatula pawokhawa nʼchiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abimeleke anati kwa Abrahamu, Nanga ana a nkhosa akazi asanu ndi awiri amene wapatula pa okha?