Genesis 21:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mwana wa Abrahamuyo, mwana amene Sara adamubalirayo, Abrahamu adamutcha Isaki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abrahamu anamutcha dzina lake la mwana wake wamwamuna amene anabala iye, amene anambalira iye Sara, Isaki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abrahamu anapereka dzina loti Isake kwa mwana wamwamuna amene Sara anamuberekera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abrahamu anamucha dzina lace la mwana wace wamwamuna amene anabala iye, amene anambalira iye Sara, Isake.