Genesis 21:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abrahamu nkuti ali wa zaka 100 pamene Isakiyo adabadwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abrahamu anali wa zaka zana limodzi pamene anambadwira iye Isaki mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abrahamu anali ndi 100 pamene mwana wake Isake anabadwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abrahamu anali wa zaka zana limodzi pamene anambadwira iye Isake mwana wace.