Genesis 22:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adasolola mpeni kuti amuphe mwana wakeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abrahamu anatambasula dzanja lake, natenga mpeni kuti amuphe mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Abrahamu anatambasula dzanja lake natenga mpeni kuti aphe mwana wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abrahamu anatambasula dzanja lace, natenga mpeni kuti amuphe mwana wace.