Genesis 22:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mngelo wa Chauta uja adamuitana Abrahamu kachiŵiri kuchokera kumwamba, adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mthenga wa Yehova anamuitana Abrahamu ndi mau odzera kumwamba kachiwiri,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mngelo wa Yehova anayitana Abrahamu kuchokera kumwamba kachiwiri
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mthenga wa Yehova anamuitana Abrahamu ndi mau odzera kumwamba kaciwiri,