Genesis 22:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku lachitatu lake Abrahamu adaona malowo chapatali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lachitatu Abrahamu anatukula maso ake naona malowo patali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lachitatu, Abrahamu anakweza maso ake ndipo anaona malowo chapatali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lacitatu Abrahamu anatukula maso ace naona malowo patari.