Genesis 23:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ahiti amene anali pamsonkhanopo adachitira umboni kuti dera lonselo ndi la Abrahamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
inalimbitsidwa kwa Abrahamu ikhale yake, pamaso pa ana a Hiti, pa onse amene analowa pa chipata cha mudzi wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kwa Abrahamu ngati chuma chake pamaso pa anthu onse a ku Hiti amene anabwera ku chipata cha mzindawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
inalimbitsidwa kwa Abrahamu ikhale yace, pamaso pa ana a Heti, pa onse amene analowa pa cipata ca mudzi wace.