Genesis 23:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adasiya mtembo wa mkazi wakewo, nakalankhula ndi anthu a ku Hiti kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abrahamu anauka pa wakufa wake, nanena kwa ana a Hiti, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Abrahamu ananyamuka pamene panali mtembo wa mkazi wakepo kupita kukayankhula ndi anthu a ku Hiti. Ndipo anati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abrahamu anauka pa wakufa wace, nanena kwa ana a Heti, nati,