Genesis 23:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Timvereni, mbuyathu. Inu ndinu nduna yaikulu pakati pathu pano. Mkazi wanuyu, mumuike m'manda aliwonse abwino amene tili nawo. Palibe ndi mmodzi yemwe pakati pathu pano amene angakumaneni manda amene tili nawo, kapena kukuletsani kuikamo amaiŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mutimvere ife mfumu, ndinu kalonga wamkulu pakati pa ife; muike wakufa wanu m'manda mwathu mosankhika: palibe munthu yense wa ife adzakaniza manda ake, kuti muike wakufa wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tatimverani mbuye wathu, inu ndinu mwana wa mfumu wamkulu pakati pathu. Chonde ikani thupi la mkazi wanu mʼmanda aliwonse amene mungafune. Palibe mmodzi wa ife amene adzakukanizani manda ake kuti musayike mkazi wanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mutimvere ife mfumu, ndinu karonga wamkuru pakati pa ife; muike wakufa wanu m'manda mwathu mosankhika: palibe munthu yense wa ife adzakaniza manda ace, kuti muike wakufa wanu.