Genesis 24:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono wantchitoyo adatenga ngamira khumi za mbuye wake, ndi mphatso zambiri zamtengowapatali, ndipo adapita ku mzinda wa Nahori, m'dziko la Mesopotamiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mnyamatayo anatenga ngamira khumi za mbuyake, namuka: chifukwa kuti chuma chonse cha mbuyake chinali m'dzanja lake: ndipo anachoka namuka ku Mesopotamiya, kumudzi wa Nahori.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono wantchito uja anatengapo ngamira khumi mwa ngamira za mbuye wake pamodzi ndi zinthu zabwino za mitundumitundu. Ndipo ananyamuka kupita ku mzinda wa Nahori, mʼdziko la Mesopotamiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mnyamatayo anatenga ngamila khumi za mbuyace, namuka: cifukwa kuti cuma conse ca mbuyace cinali m'dzanja lace: ndipo anacoka namuka ku Mesopotamiya, ku mudzi wa Nahori.