Genesis 24:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndili pano pa chitsime, ndipo akazi amumzindamu abwera kudzatunga madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ine ndiima pa chitsime cha madzi; ndipo ana akazi a m'mudzi atuluka kudzatunga madzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani ndayima pambali pa chitsimechi, ndipo atsikana a mu mzindawu akubwera kudzatunga madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ine ndiima pa citsime ca madzi; ndipo ana akazi a m'mudzi aturuka kudzatunga madzi;