Genesis 24:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mlendo uja atamwa madziwo, namwaliyo adati, “Ndibwera nawonso madzi, kuti zimwe ngamira zanu mpaka zikwane.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atatha kumwetsa iye, anati, Ndidzatungiranso ngamira zako, mpaka zitamwa zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atatha kupereka madzi akumwa kwa mlendo uja, mtsikanayo anati, “Ndikatungiranso ngamira madzi kuti zimwe mpaka zitakwana.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atatha kumwetsa iye, anati, Ndidzatungiranso ngamila zako, mpaka zitamwa zonse.