Genesis 24:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu uja anali phee, kuyang'ana zimene ankachita namwaliyo, kuti aone ngati Chauta wadalitsa ulendo wake kapena ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthuyo ndipo anamyang'anira iye, nakhala chete, kuti adziwe ngati Yehova anamuyendetsa bwino kapena iai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Modekha, munthu uja anayangʼanitsitsa kwambiri mtsikana uja kuti adziwedi ngati Yehova anamutsogolera pa ulendo wake uja kapena ayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthuyo ndipo anamyang'anira iye, nakhala cete, kuti adziwe ngati Yehova anamuyendetsa bwino kapena iai.