Genesis 24:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adafunsa namwaliyo kuti, “Kodi atate anu ndani? Tandiwuzani chonde. Kodi alipo malo oti ine ndi anzangaŵa nkugonako usiku uno?” Namwaliyo adayankha kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati, Ndiwe mwana wa yani? Undiuzetu. Kodi kunyumba ya atate wako kuli malo akuti tigoneko ife?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anafunsa namwaliyo kuti, “Chonde tandiwuza, kodi ndiwe mwana wa yani? Ndipo kodi malo alipo kwanu woti ife nʼkugona?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati, Ndiwe mwana wa yani? Undiuzetu. Kodi ku nyumba ya atate wako kuli malo akuti tigoneko ife?