Genesis 24:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chakudya chodyetsa nyamazi chiliko kwathu, ndipo malo oti inu mugoneko aliponso.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natinso kwa iye, Tili nao udzu ndi zakudya zambiri ndi malo ogona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anapitiriza kunena kuti, “Chakudya chodyetsa nyamazi chilipo kwathu ndipo malo woti mugone aliponso.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Natinso kwa iye, Tiri nao maudzu ndi zakudya zambiri oeli malo ogona.