Genesis 24:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono namwali uja adathamangira kunyumba kwa mai wake, nafotokozera onse nkhani yonseyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namwaliyo ndipo anathamanga nawauza zimenezo kunyumba ya amake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtsikana uja anathamanga nakafotokozera zimenezi anthu a kwa amayi ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namwaliyo ndipo anathamanga nawauza zimenezo ku nyumba ya amace.