Genesis 24:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikufuna kuti ulumbire pamaso pa Chauta, Mulungu wa dziko lakumwamba ndi dziko lapansi, kuti sudzamufunira mbeta mwana wanga pakati pa atsikana Achikanani kuno ndili ine kuno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndidzakulumbiritsa iwe pa Yehova, Mulungu wa Kumwamba, ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti usadzamtengere mwana wanga mkazi wa kwa ana akazi a Akananiwo, amene ndikhala pakati pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikufuna kuti ulumbire pamaso pa Yehova, Mulungu wakumwamba ndi dziko lapansi, kuti sudzamupezera mwana wanga mkazi pakati pa atsikana Achikanaani a kuno kumene ndikukhala,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndidzakulumbiritsa iwe pa Yehova, Mulungu wa Kumwamba, ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti usadzamtengere mwana wanga mkazi wa kwa ana akazi a Akananiwo, amene ndikhala pakati pao.