Genesis 24:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mbuyanga adandilumbiritsa kuti ndisunge mau ake akuti, ‘Mwana wangayu usadzamfunire mbeta pakati pa anamwali a dziko lino la Kanani, kumene ndili ine kuno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mbuyanga anandilumbiritsa ine kuti, Usamtengere mwana wanga mkazi wa ana akazi a Kanani, m'dziko mwao m'mene ndikhala ine;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mbuye wanga anandilumbiritsa kuti ndisunge mawu ake akuti, ‘Usadzamupezere mwana wanga mkazi kuchokera mwa atsikana a dziko lino la Kanaani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mbuyanga anandilumbiritsa ine kuti, Usamteogere mwana wanga mkazi wa ana akazi a Kanani, m'dziko mwao m'mene ndikhala ine;