Genesis 24:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma upite kwathu kwa atate anga ndi achibale anga, kukamutengera mkazi mwana wanga kumeneko.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma udzanke kunyumba ya atate wanga, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga mkazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma upite ku banja la abambo anga ndi kwa abale anga kuti ukamupezere mkazi mwana wanga.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma udzanke ku nyumba ya atate wanga, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga mkazi.