Genesis 24:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo ine ndidamuyankha mbuyanga kuti, ‘Nanga zidzatani ngati mkaziyo adzakana kubwera nane kuno?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinati kwa mbuyanga, Kapena mkazi sadzanditsata ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndipo ine ndinati kwa mbuye wanga, ‘Nanga mkaziyo akakapanda kubwera nane pamodzi?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinati kwa mbuyanga, Kapena mkazi sadzanelitsata ine.