Genesis 24:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma udzapita ku dziko lakwathu, ndipo ukamutengera mkazi mwana wanga kumeneko pakati pa abale anga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma udzanke ku dziko langa, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga Isaki mkazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma kuti udzapita ku dziko la kwathu ndi kukamupezera mkazi mwana wanga Isake pakati pa abale anga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma udzanke ku dziko langa, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga Isake mkazi.