Genesis 24:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukachita zimenezi, matemberero anga sadzakugwera. Koma iweyo utafika ku banja langalo, anthu angawo nakakukana, udzamasuka ku lumbiro lako.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ukatero udzakhala wosachimwa pa malumbiro ako, pofika iwe kwa abale anga; ndipo ngati sadzakupatsa iwe, udzakhala wosachimwa pa malumbiro ako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukadzachita zimenezi udzakhala mfulu wosamangidwa ndi lumbiro langali. Koma tsono ukadzafika kwa fuko langa, ndipo ngati sadzalola kukupatsa mbeta ya mwana wanga, aponso udzamasuka ku lumbiro langali.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ukatero udzakhala wosacimwa pa malumbiro ako, pofika iwe kwa abate anga; ndipo ngati sadzakupatsa iwe, udzakhala wosacimwa pa malumbiro ako.