Genesis 24:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndili pano pachitsime, pakabwera namwali pano kudzatunga madzi, ine ndidzampempha kuti: Chonde patseko madzi a mumtsuko mwako kuti ndimwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
taonani, ine ndiima pa kasupe wa madzi, ndipo pakhale, kuti namwali amene atuluka kudzatunga madzi ndimwe pang'ono m'mtsuko mwako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
taonani ndayima pambali pa chitsime ichi; ndipo ndidzati kwa namwali amene atabwere kudzatunga kuti, chonde nditamwako madzi a mu mtsuko wakowu,’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
taonani, ine ndiima pa kasupe wa madzi, ndipo pakhale, kuti namwali amene aturuka kudzatunga madzi, ndikati kwa iye, Ndipatse madzi ndimwe pang'ono m'mtsuko mwako;