Genesis 24:52 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wantchito wa Abrahamu uja atamva mau ao aja, adaŵeramitsa mutu napembedza Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali pamene anamva mauwo mnyamata wa Abrahamu, anamgwadira Yehova pansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wantchito wa Abrahamu uja atamva zimene anawerama pansi pamaso pa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali pamene anamva mauwo mnyamata wa Abrahamu, anamgwadira Yehova pansi,