Genesis 24:57 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo iwowo adayankha kuti, “Tiyeni timuitane namwaliyo, kuti timve zimene iyeyo anene.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati iwo, Tidzamuitana namwaliyo, tidzamfunsa pakamwa pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma iwo anati, “Bwanji timuyitane mtsikanayo ndipo timufunse ngati afuna kupita nanu panopa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati iwo, Tidzamuitana namwaliyo, tidzamfunsa pakamwa pace.