Genesis 24:59 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adamlola Rebeka pamodzi ndi mlezi wake, kuti apite ndi wantchito wa Abrahamu ndi anthu aja omuperekezaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamlola Rebeka mlongo wao ndi mlezi wake, amuke pamodzi ndi mnyamata wake wa Abrahamu, ndi anthu ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anamulola Rebeka pamodzi ndi mlezi wake kuti apite ndi wantchito wa Abrahamu pamodzi ndi anthu amene anali naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamlola Rebeka mlongo wao ndi mlezi wace, amuke pamodzi ndi mnyamata wace wa Abrahamu, ndi anthu ace.