Genesis 24:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abrahamu adayankha kuti, “Usadzamperekeze kumeneko mwana wangayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abrahamu anati kwa iye, Chenjera iwe, usambwezerenso mwana wanga kumeneko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abrahamu anati, “Uwonetsetse kuti usadzabwerere naye mwana wanga kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abrahamu anati kwa iye, Cenjera iwe, usambwezerenso mwana wanga kumeneko.