Genesis 24:62 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Isaki anali atachoka kuchipululu kumene kunali chitsime cha Wamoyo-Wondipenya chija, kukakhala m'chigawo chakumwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Isaki anadzera njira ya Beere-Lahai-Roi; chifukwa kuti anakhala iye m'dziko la kumwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawiyi nʼkuti Isake atafika kuchokera ku chitsime cha Wamoyo Wondipenya (Beeri-lahai-roi), popeza tsopano ankakhala ku Negevi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Isake anadzera njira ya Beereahai-roi; cifukwa kuti anakhala iye n'dziko la kumwera.