Genesis 27:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukapereke chakudyacho kwa bambo wako kuti akadye, ndipo akudalitse asanafe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo udzapita nacho kwa atate wako, kuti adye, ndi kukudalitsa iwe asanafe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka upite nacho chakudyacho kwa abambo ako kuti adye ndi kukudalitsa asanafe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo udzapita naco kwa atate wako, kuti adye, ndi kukudalitsa iwe asanafe,