Genesis 27:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwina mwake bambo wanga adzandikhudza, ndipo adzadziŵa kuti ndikumunyenga. Motero m'malo mondidalitsa, adzanditemberera.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kapena atate wanga adzandiyambasa, ndipo ndidzaoneka pamaso pake ngati wakunyenga; pamenepo ndidzadzitengera ine temberero, si mdalitso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwina abambo anga adzandikhudza, ndipo ndidzaoneka kuti ndawapusitsa. Tsono ndizadzitengera temberero mʼmalo mwa madalitso.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena atate wanga adzandiyambasa, ndipo ndidzaoneka pamaso pace ngati wakunyenga; pamenepo ndidzadzitengera ine temberero, si mdalitso.