Genesis 27:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adapita kwa bambo wake, namuitana kuti, “Bambo!” Isaki adafunsa kuti, “Kodi ndiwe mwana wanga uti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye analowa kwa atate wake, nati, Atate wanga; iye anati, Ndine pano; ndani iwe mwana wanga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anapita kwa abambo ake ndipo anati, “Abambo anga.” Ndipo anayankha, “Eya, kodi ndiwe mwana wanga uti?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye analowa kwa atate wace, nati, Atate wanga; iye anati, Ndine pano; ndani iwe mwana wanga?