Genesis 27:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adasendera pafupi ndi bambo wake, ndipo bambo wakeyo adamukhudza nati, “Liwuli ndi la Yakobe, koma mikonoyi ndi ya Esau.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anasendera kwa Isaki atate wake, ndipo anamyambasa nati, Mau ndi mau a Yakobo, koma manja ndi manja a Esau.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anasendera kufupi ndi abambo ake Isake ndipo anamukhudza nati, “Mawuwa ndi mawu a Yakobo koma mikonoyi ndi mikono ya Esau.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo anasendera kwa Isake atate wace, ndipo anamyambasa nati, Mau ndi mau a Yakobo, koma manja ndi manja a Esau.