Genesis 27:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu akugwetsere mvula, ndipo minda yako ikhale yobala bwino. Akupatse zakudya ndi zakumwa zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu akupatse iwe mame a kumwamba, ndi zonenepa za dziko lapansi, ndi tirigu wambiri ndi vinyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu akugwetsere mame akumwamba ndipo minda yako ibale tirigu wambiri ndi vinyo watsopano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mlungu akupatse iwe mame a kumwamba, Ndi zonenepa za dziko lapansi, Ndi tirigu wambiri ndi vinyo;