Genesis 27:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tenga zida zako, uta ndi mivi yomwe, upite ku thengo ukandiphere nyama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsopano tengatu zida zako ndi phodo lako ndi uta wako, numuke kuthengo kundisakira ine nyama:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono tenga zida zako, muvi wako ndi uta, pita kuthengo ukandiphere nyama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
tsopano tengatu zida zako ndi phodo lako ndi uta wako, numuke kuthengo kundisakira ine nyama;