Genesis 27:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Esau adapitirirabe kumpempha bambo wakeyo kuti, “Kodi bambo, dalitso muli nalo limodzi lokhali? Tandidalitsaniko nanenso bambo.” Ndipo atatero adayambanso kulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Esau anati kwa atate wake, Kodi muli nao mdalitso umodzi wokha, atate wanga? Mundidalitse ine, inenso, atate wanga. Ndipo Esau anakweza mau ake nalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Esau anati kwa abambo ake, “Kodi muli ndi dalitso limodzi lokhali, abambo anga? Inenso mundidalitse chonde abambo anga!” Pomwepo Esau analira mokuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Esau anati kwa atate wace, Kodi muli nao mdalitso umodzi wokha, atate wanga? Mundidalitse ine, inenso, atate wanga, Ndipo Esau anakweza mau ace nalira.