Genesis 27:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Undiphikire chakudya chokoma chija ndimakondachi, ubwere nacho kuno. Nditadya, ndidzakudalitsa ndisanafe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nundikonzere ine chakudya chokolera chonga chomwe ndichikonda ine, nudze nacho kwa ine kuti ndidzadye; kuti moyo wanga ukadalitse iwe ndisanafe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Undikonzere chakudya chabwino monga muja ndimakonderamu ndipo ubwere nacho kwa ine kuti ndidye ndi kuti ndikudalitse ndisanamwalire.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nundikonzere ine cakudya cokolera conga comwe ndicikonda ine, nudze naco kwa ine kuti ndidzadye; kuti moyo wanga ukadalitse iwe ndisanafe.