Genesis 27:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsopano mwana wanga, uchite zimene ndikuuze. Konzeka, thaŵira kwa mlongo wanga Labani ku Harani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano mwana wanga, tamvera mau anga: tauka, nuthawire kwa Labani mlongo wanga ku Harani;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano mwana wanga, chita zimene ndinene: Nyamuka tsopano, uthawire kwa mlongo wanga Labani ku Harani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopane mwana wanga, tamvera mau anga: tauka, nuthawire kwa Labani mlongo wanga ku Harana;