Genesis 27:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bakakhala kwa iyeyo kanthaŵi ndithu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ukhale naye masiku akuwerengeka, mpaka wamchokera ukali wa mkulu wako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukakhale naye kwa kanthawi mpaka mkwiyo wa mʼbale wako utatsika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ukhale naye masiku akuwerengeka, mpaka wamcokera ukali wa mkuru wako;