Genesis 27:46 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rebeka adauza Isaki kuti, “Akazi Achihitiŵa, ine ndatopa nawo! Yakobenso akakwatira wina mwa a Ahiti akunoŵa, ine kodi moyo wanga nkukomanso?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati Rebeka kwa Isaki, Ndalema moyo wanga chifukwa cha ana akazi a Heti: akatenga Yakobo mkazi wa ana akazi a Heti, onga ana akazi a m'dziko lino, moyo wanga udzandikhalira ine bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Rebeka anati kwa Isake, “Ine sindikukondwera nawo anamwali a Chihiti. Ndipo ngati Yakobo angapeze mbeta kuno mwa anamwali a Chihitiwa, ndiye kuli bwino kungofa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati Rebeka kwa Isake, Ndalema moyo wanga cifukwa ca aria akazi a Heti: akatenga Yakobo mkazi wa ana akazi a Heti, onga ana akazi a m'dziko lino, moyo wanga udzandikhalira ine bwanji?