Genesis 28:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adachita mantha, nanena kuti, “Hi, malo ano ndi oopsa! Zoonadi pano mpa nyumba ya Mulungu ndiponso khomo la kumwamba.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaopa, nati, Poopsa pompano! Pompano ndipo pa nyumba ya Mulungu, si penai, pompano ndipo pa chipata cha kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anachita mantha ndipo anati, “Malo ano ndi woopsa ndithu. Zoonadi pano ndi pa nyumba ya Mulungu ndi khomo la kumwamba.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaopa, nati, Poopsya pompano! pompano ndipo pa nyumba ya Mulunga, si penai, pompano ndipo pa cipata ca kumwamba.