Genesis 28:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndi kundibwezera bwino kwathu kwa atate anga, mudzakhala Mulungu wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ndibwerenso kunyumba ya atate wanga ndi mtendere, pamenepo Yehova adzakhala Mulungu wanga,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati inu mudzandibweretsa kwathu mu mtendere, ndiye kuti mudzakhala Mulungu wanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti ndibwerenso ku nyumba ya atate wanga ndi mtendere, pamenepo Yehova adzakhala Mulungu wanga,