Genesis 28:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamva kuti Yakobe wamvera bambo wake ndi mai wake, ndipo kuti wapita ku Mesopotamiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiponso kuti Yakobo anamvera atate wake ndi amake, nanka ku Padanaramu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anamvera abambo ake ndi amayi ake ndi kupita ku Padanaramu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiponso kuti pamene anamdalitsa iye, anamuuza iye kuti, Usatenge mkazi wa ana akazi a Kanani; ndiponso kuti Yakobo anamvera atate wace ndi amace, nanka ku Padanaramu;