Genesis 29:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yakobe adapitirira ulendo wake, kupita ku dziko la anthu akuvuma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo ananka ulendo wake, nafika ku dziko la anthu a kum'mawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anapitiriza ulendo wake kupita ku dziko la anthu a kummawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo ananka ulendo wace, nafika ku dziko la anthu a kum'mawa.