Genesis 29:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Labani adamuuza kuti, “Inde, zoonadi, iwe ndiwe mbale wanga weniweni.” Yakobe adakhala kumeneko mwezi wathunthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Labani anati kwa iye, Etu, iwe ndiwe fupa langa ndi thupi langa. Ndipo anakhala naye nthawi ya mwezi umodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo, Labani anati kwa iye, “Iwe ndiwe ndithu fupa ndi mnofu wanga.” Yakobo anakhala ndi Labani mwezi umodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Labani anati kwa iye, Etu, iwe ndiwe pfupa langa ndi thupi langa. Ndipo anakhala naye nthawi ya mwezi umodzi.