Genesis 29:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Labani anali ndi ana aakazi aŵiri, wamkulu Leya, wamng'ono Rakele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Labani anali ndi ana akazi awiri, dzina la wamkulu ndi Leya, dzina la wamng'ono ndi Rakele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Labani anali ndi ana aakazi awiri; dzina la wamkulu linali Leya, ndipo dzina la wamngʼono linali Rakele.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Labani anali ndi ana akazi awiri, dzina la wamkuru ndi Leya, dzina la wamng'ono ndi Rakele.