Genesis 29:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Leya anali ndi maso ofooka, koma Rakele anali chiphadzuŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maso a Leya anali ofooka, koma Rakele anali wokoma thupi ndi wokongola.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Leya anali ndi maonekedwe wofowoka koma Rakele anali wa maonekedwe wokongola kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maso a Leya anali ofok a, koma Rakele anali wokoma thupi ndi wokongola.