Genesis 29:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma usiku umenewo Labani adatenga Leya m'malo mwa Rakele nampatsa Yakobe, ndipo Yakobe adaloŵana ndi Leya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali madzulo Labani anatenga Leya mwana wake wamkazi, nadza naye kwa Yakobo, ndipo iye analowa kwa mkaziyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pokwana usiku, Labani anatenga mwana wake wamkazi Leya namupatsa Yakobo, ndipo Yakobo anagona naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali madzulo Labani anatenga Leya mwana wace wamkazi, nadza naye kwa Yakobo, ndipo iye analowa kwa mkaziyo.