Genesis 29:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake kutacha, Yakobe adaona kuti mkaziyo ndi Leya. Tsono adafunsa Labani kuti, “Chifukwa chiyani mwandichita zotere? Kodi suja ndidakugwirirani ntchito kuti ndikwatire Rakele? Chifukwa chiyani tsono mwandinyenga?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali m'mamawa, anaona kuti ndi Leya; ndipo anati kwa Labani, Chiyani wandichitira ine? Kodi sindinakutumikira iwe chifukwa cha Rakele? Wandinyenga ine bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakucha mmawa, Yakobo anaona kuti anagona ndi Leya. Choncho Yakobo anafunsa Labani, “Nʼchiyani mwandichitirachi? Kodi ine sindinakugwirireni ntchito chifukwa cha Rakele? Bwanji mwandinyenga?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali m'mamawa, anaona kuti ndi Leya; ndipo anati kwa Labani, Ciani wandicitira ine? Kodi sindinakutumikira iwe cifukwa ca Rakele? wandinyenga ine bwanji?