Genesis 29:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Labani adayankha kuti, “Si mwambo wathu kuno kukwatitsa wamng'ono, mkulu wake asanakwatiwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Labani anati, Satero kwathu kuno, kupatsa wamng'ono asanapatse wamkulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Labani anayankha, “Si mwambo wathu kuno kupereka wamngʼono ku banja, wamkulu asanakwatiwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Labani anati, Satero kwathu kuno, kupatsa wamng'ono asanapatse wamkuru.