Genesis 29:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adavomera, ndipo mlungu wa chikondwerero chaukwati utapita, Labani adapereka Rakele kwa Yakobe kuti akhale mkazi wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yakobo ndipo anachita chotero namaliza sabata lake; ndipo Labani anampatsa iye Rakele mwana wake wamkazi kuti akwatire iyenso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anachitadi momwemo. Anamaliza sabata ya chikondwerero cha Leya, ndipo Labani anamupatsa Rakele kuti akhale mkazi wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yakobo ndipo anacita cotero namariza sabata lace; ndipo Labani anampatsa iye Rakele mwana wace wamkazi kuti akwatire iyenso.